This article was originally published on Malawi24, Malawi's #1 independent news platform.
Nanga angalime? Ayitu, madobadobawo ntchito ndiyomweyo. Komabe, kuyambira lero lolemba akuyenera kupeza dimba poti nduna yanenetsa kuti iwaonetsa chidameta nkhanga mpala. Wachiwiri kwa nduna yachitetezo mdziko, Norman Chisale walengeza kuti kuyambira lero lolemba, madobadoba omwe amapezeka ku maofesi a nthambi yopanga ziphaso zoyendera sadzapezekaso. Poyankhula loweruka, Chisale wati ena mwa mavuto omwe anthu akukumana nawo […]
Read the full article and more Malawi news at Malawi24 — Breaking news, politics, business, sport and entertainment from Malawi and Africa, updated 24/7.